settings icon
share icon

Takulandirani ku Chichewa cha www.GotQuestions.org!

Mafunso a Baibulo oyankhidwa

Tikupepesa, koma sitingalore mafunso amene atumizidwa kwa ife olembedwa m’Chichewa panopa. Ngati mungalembe ndikuwerenga Chingerezi, mukhonza kutumiza mafunso anu ku - https://www.gotquestions.org/Bible-Questions.html.

Mndandanda uli m’musiwu ndiwamapeji amene tili nawo m’Chichewa:Uthenga Wabwino

Munalandira Moyo Wosatha?

Mwakhululukidwa? Ndingakhululukidwe bwanji ndi Mulungu?

Zikutanthauza chiyani kuvomera Yesu ngati Mpulumutsi wa umoyo wako?

Kodi domgosolo la chipulumutso ndilotani / njira ya chipulumutso?

Kodi m’Khristu ndi chiyani?

Kodi citanthauza ciani kukhala Mkristu wobadwa kwa tsopano? Kodi ndingabadwe bwanji kwa tsopano?

Kodi malamulo anai a zauzimu ndi otani?

Ndingakhale bwanji bwino ndi Mulungu?

Kodi Yesu ndiye njira yokha yopita Kumwamba?

Kodi ndingadziwe bwanji motsimikiza kuti ndikafa ndidzapita Kumwamba?

Kodi munthu akafa, akhalanso ndi moyo?

Kodi cipembedzo coona ndi citi kwa ine?

Kodi Njira ya Aroma yopita ku cipulumutso ndi ciani?

Kodi pemphero la munthu ocimwa nciani?

Ndangoyika chikhulupiliro changa mwa Yesu… Tsopano?Mafunso ofunikira kwambiri

Kodi Mulungu alipo? Pali umboni kuti Mulungu alipo?

Kodi Yesu Khristu ndiye yani?

Kodi Yesu ndi Mulungu? Kodi Yesu ananenapo kuti Iye ndi Mulungu?

Kodi makhalidwe a Mulungu ndi otani? Kodi Mulungu ali bwanji?

Kodi Baibulo ndilo Mau a Mulungu zoonadi?

Kodi Cikristu nciani ndipo Akristu amakhulupirira ciani?

Kodi Akristu ayenera kumvera lamulo la mu Cipangano Cakale?

Kodi umulungu wa Yesu upezeka mu Baibulo?

Kodi cipulumutso citheka ndi cikhulupiriro cokha kapena cikhulupiriro ndi zinchito?

Kodi Mzimu Woyera ndani?

Kodi Mulungu ndi oona? Kodi ndingadziwe bwanji kuti Mulungu ndi oona?

Kodi ndingadziwe bwanji cifuniro ca Mulungu mu moyo wanga? Kodi Baibulo linena ciani pa zakudziwa cifuniro ca Mulungu?

Kodi tanthauzo la moyo nciani?” Kodi ndingapeze bwanji tanthauzo la moyo wanga?

Ndingathe bwanji kugonjetsa cimo mu umoyo wanga wa CiKristu?

Cifukwa ninji sindiyenera kudzipha?Mafunso ofunsidwa kawirikawiri

Cimacitika nciani potsatira imfa?

Kodi Baibulo linena ciani pa kumwa zoledzeretsa / vinyo (waini)? Kodi ndi cimo kwa Mkristu kumwa zoledzeretsa / vinyo (waini)?

Kodi mkazi wa Kaini anali ndani? Kodi mkazi wa Kaini anali mlongo wace?

Kodi ubatizo wa Cikristu ndiwofunikira motani?

Kodi Baibulo linena ciani za kupereka ca khumi?

Kodi Baibulo linena ciani za madainasosi? Kodi madainasosi alimo mu Baibulo?

Kodi Baibulo linena ciani pa za kulekana pa banja ndi kukwatiranso kapena kukwatiriwanso?

Kodi cisamaliro cosatha cipezeka mu Baibulo?

Kodi mpikisano wobecha (njuga, kasino, lotare, jakipoti ndi zina) ndi cimo? Kodi Baibulo linena ciani za mpikisano wobecha?

Kodi Baibulo linena ciani za mcitidwe wokonda zogonana wa pakati pa akazi kapena amuna okhaokha? Kodi mcitidwe wokonda zogonana wa pakati pa akazi kapena amuna okhaokha ndi cimo?

Kodi Baibulo linena ciani za cikwati pakati pa osiyana mitundu (osiyana khungu)?

Kodi Yesu atafa anali kuti asanaukitsidwe pa masiku atatu aja a pakati pa imfa yace ndi kuukitsidwa kwace?

Kuzithetsa nyere – Kodi ndi cimo monga mwa Baibulo?

Okapulumutsidwa kamodzi, ukhalabe wopulumutsidwa?

Kodi ziweto / nyama zimapita Kumwamba? Kodi ziweto / nyama zili ndi mizimu?

Kodi Baibulo linena ciani pa kukhala m’cikondi munthu asanakwatire kapena asanakwatiridwe / kumacita zogonana asanakhale m’banja?

Kodi mphatso yakulankhula mu malilime ndi ciani?

Kodi a Kristu anenapo bwanji pa nkhani za kudzipha wekha? Kodi Baibulo linena ciani pakudzipha wekha?

Kodi Baibulo linena ciani pa za kuzitema kapena kuzilembalemba mphini pa thupi kapenanso kuziboola pa thupi?

Kodi baibulo liphunzitsa ciani za Mulungu m’modzi mwa atatu?

Azibusa acikazi / wolalikira? Kodi Baibulo linena ciani pa akazi mu ulaliki?

Mafunso a Baibulo oyankhidwa
Facebook icon Twitter icon Pinterest icon Email icon
© Copyright Got Questions Ministries